2 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Ataliya,+ mayi wa Ahaziya+ ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu.+ 2 Mbiri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, iye analimbitsa ufumu wake. Chotero anapha abale ake+ onse ndi lupanga ndiponso akalonga ena a Isiraeli.
4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, iye analimbitsa ufumu wake. Chotero anapha abale ake+ onse ndi lupanga ndiponso akalonga ena a Isiraeli.