Salimo 78:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+
34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+