Numeri 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo ataona zimenezo, anapita kwa Mose n’kumuuza kuti: “Tachimwa ife,+ chifukwa talankhula mowiringula kwa Yehova ndiponso kwa inuyo. Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.”+ Pamenepo Mose anayamba kuwapepesera kwa Mulungu.+ Oweruza 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Isiraeli anayamba kulirira Yehova,+ chifukwa Yabini anawapondereza+ kwambiri zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+
7 Anthuwo ataona zimenezo, anapita kwa Mose n’kumuuza kuti: “Tachimwa ife,+ chifukwa talankhula mowiringula kwa Yehova ndiponso kwa inuyo. Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.”+ Pamenepo Mose anayamba kuwapepesera kwa Mulungu.+
3 Ana a Isiraeli anayamba kulirira Yehova,+ chifukwa Yabini anawapondereza+ kwambiri zaka 20, ndipo iye anali ndi magaleta ankhondo 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+