Salimo 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+ Habakuku 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndidzakondwerabe mwa Yehova+ ndipo ndidzasangalala mwa Mulungu wachipulumutso changa.+ Afilipi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye.+ Ndibwerezanso, Kondwerani.+
33 Fuulani mosangalala chifukwa cha Yehova, inu nonse olungama.+M’poyenera kuti owongoka mtima atamande Mulungu.+