Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+

      Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+

      Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+

  • Salimo 72:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+

      Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+

  • Salimo 86:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+

      Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+

  • Salimo 89:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pakuti ndani kumwamba angayerekezeredwe ndi Yehova?+

      Ndani angafanane ndi Yehova pakati pa ana a Mulungu?+

  • Yesaya 40:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+

  • Yeremiya 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kodi ndani amene sangakuopeni,+ inu Mfumu ya mitundu yonse?+ Inuyo ndinu woyenera kuopedwa, chifukwa chakuti pakati pa anzeru onse a m’mitundu ya anthu ndiponso pakati pa maufumu awo onse, palibiretu aliyense wofanana ndi inu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena