Salimo 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu Mulungu, chilungamo chanu chili ngati mapiri anu.+Chiweruzo chanu ndi chozama kwambiri ngati madzi akuya.+Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+ Salimo 57:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwakukulu ndipo kwafika kumwamba,+Choonadi chanu chafika kuthambo.+ Salimo 89:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+
6 Inu Mulungu, chilungamo chanu chili ngati mapiri anu.+Chiweruzo chanu ndi chozama kwambiri ngati madzi akuya.+Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+
10 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwakukulu ndipo kwafika kumwamba,+Choonadi chanu chafika kuthambo.+
14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+