Salimo 145:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova amakomera mtima aliyense,+Ndipo ntchito zake zonse amazichitira chifundo.+ Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapatsa zilombo chakudya chawo,+Amapatsanso ana a makwangwala chakudya chimene amalirira.+ 1 Timoteyo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa chifukwa chimenechi, tikugwira ntchito mwakhama ndiponso mwamphamvu,+ chifukwa chiyembekezo+ chathu chili mwa Mulungu wamoyo, amene ali Mpulumutsi+ wa anthu a mtundu uliwonse,+ koma makamaka okhulupirika.+
10 Pa chifukwa chimenechi, tikugwira ntchito mwakhama ndiponso mwamphamvu,+ chifukwa chiyembekezo+ chathu chili mwa Mulungu wamoyo, amene ali Mpulumutsi+ wa anthu a mtundu uliwonse,+ koma makamaka okhulupirika.+