Salimo 104:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zonsezi zimayembekezera inu+Kuti muzipatse chakudya pa nyengo yake.+ Salimo 136:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amenenso amapereka chakudya kwa zamoyo zonse:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Salimo 145:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+
25 Amenenso amapereka chakudya kwa zamoyo zonse:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Salimo 145:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+
15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+