Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kwa nyama iliyonse yam’tchire ya padziko lapansi, ndi kwa cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, komanso kwa chokwawa chilichonse cha padziko lapansi chimene chili ndi moyo, ndapereka zomera zonse kuti zikhale chakudya chawo.”+ Ndipo zinaterodi.

  • Salimo 104:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Zonsezi zimayembekezera inu+

      Kuti muzipatse chakudya pa nyengo yake.+

  • Salimo 136:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Amenenso amapereka chakudya kwa zamoyo zonse:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Mateyu 24:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 “Ndani kwenikweni amene ali kapolo wokhulupirika ndi wanzeru+ amene mbuye wake anamuika kuti aziyang’anira antchito ake apakhomo, ndi kuwapatsa chakudya pa nthawi yoyenera?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena