Salimo 104:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zonsezi zimayembekezera inu+Kuti muzipatse chakudya pa nyengo yake.+ Salimo 145:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+ Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapatsa zilombo chakudya chawo,+Amapatsanso ana a makwangwala chakudya chimene amalirira.+ Mateyu 5:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 kuti musonyeze kuti ndinudi ana a Atate wanu wakumwamba.+ Chifukwa iye amawalitsira dzuwa lake pa anthu oipa ndi abwino, ndi kuvumbitsira mvula anthu olungama ndi osalungama omwe.+
15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+
45 kuti musonyeze kuti ndinudi ana a Atate wanu wakumwamba.+ Chifukwa iye amawalitsira dzuwa lake pa anthu oipa ndi abwino, ndi kuvumbitsira mvula anthu olungama ndi osalungama omwe.+