Yobu 38:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya? Luka 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+
41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?
24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+