Salimo 104:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zonsezi zimayembekezera inu+Kuti muzipatse chakudya pa nyengo yake.+ Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapatsa zilombo chakudya chawo,+Amapatsanso ana a makwangwala chakudya chimene amalirira.+ Mateyu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onetsetsani mbalame+ zam’mlengalenga, pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola, kapenanso kusunga chakudya m’nkhokwe. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Nanga inu sindinu amtengo wapatali kuposa mbalame kodi?+ Luka 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+
26 Onetsetsani mbalame+ zam’mlengalenga, pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola, kapenanso kusunga chakudya m’nkhokwe. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Nanga inu sindinu amtengo wapatali kuposa mbalame kodi?+
24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+