Luka 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ganizirani za akhwangwala: Iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nkhokwe kapena nyumba yosungiramo zinthu, koma Mulungu amawadyetsa.+ Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, ptsa. 20-21 Nsanja ya Olonda,8/1/2010, tsa. 29
24 Ganizirani za akhwangwala: Iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nkhokwe kapena nyumba yosungiramo zinthu, koma Mulungu amawadyetsa.+ Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?+