Mateyu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yangʼanitsitsani mbalame zamumlengalenga,+ pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola kapenanso kusunga chakudya mʼnyumba zosungiramo zinthu. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame? Luka 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipotu ngakhale tsitsi lonse lamʼmutu mwanu amaliwerenga.+ Musachite mantha, ndinu ofunika kwambiri kuposa mpheta zambiri.+
26 Yangʼanitsitsani mbalame zamumlengalenga,+ pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola kapenanso kusunga chakudya mʼnyumba zosungiramo zinthu. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?
7 Ndipotu ngakhale tsitsi lonse lamʼmutu mwanu amaliwerenga.+ Musachite mantha, ndinu ofunika kwambiri kuposa mpheta zambiri.+