Mateyu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Onetsetsani mbalame+ zam’mlengalenga, pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola, kapenanso kusunga chakudya m’nkhokwe. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Nanga inu sindinu amtengo wapatali kuposa mbalame kodi?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, tsa. 18 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2016, ptsa. 9-10 Galamukani!,8/2014, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,6/15/2003, tsa. 319/15/1995, tsa. 329/1/1992, tsa. 2810/1/1990, ptsa. 18-192/15/1988, tsa. 12
26 Onetsetsani mbalame+ zam’mlengalenga, pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola, kapenanso kusunga chakudya m’nkhokwe. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Nanga inu sindinu amtengo wapatali kuposa mbalame kodi?+
6:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, tsa. 18 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2016, ptsa. 9-10 Galamukani!,8/2014, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,6/15/2003, tsa. 319/15/1995, tsa. 329/1/1992, tsa. 2810/1/1990, ptsa. 18-192/15/1988, tsa. 12