Mateyu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yangʼanitsitsani mbalame zamumlengalenga,+ pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola kapenanso kusunga chakudya mʼnyumba zosungiramo zinthu. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame? Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, tsa. 18 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2016, ptsa. 9-10 Galamukani!,8/2014, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,6/15/2003, tsa. 319/15/1995, tsa. 329/1/1992, tsa. 2810/1/1990, ptsa. 18-192/15/1988, tsa. 12
26 Yangʼanitsitsani mbalame zamumlengalenga,+ pajatu sizifesa mbewu kapena kukolola kapenanso kusunga chakudya mʼnyumba zosungiramo zinthu. Koma Atate wanu wakumwamba amazidyetsa. Kodi inu si amtengo wapatali kuposa mbalame?
6:26 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, tsa. 18 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2016, ptsa. 9-10 Galamukani!,8/2014, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,6/15/2003, tsa. 319/15/1995, tsa. 329/1/1992, tsa. 2810/1/1990, ptsa. 18-192/15/1988, tsa. 12