Luka 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2023, ptsa. 20-21 Nsanja ya Olonda,8/1/2010, tsa. 29
24 Onetsetsani makwangwala,+ iwo safesa mbewu kapena kukolola. Alibe nyumba yosungiramo zinthu kapena nkhokwe, komatu Mulungu amawadyetsa. Kodi inu si ofunika kwambiri kuposa mbalame?+