Salimo 71:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Tikanena za zinthu zazikulu zimene munachita,+Inu Mulungu, ndani angafanane ndi inu?+
19 Chilungamo chanu, inu Mulungu chafika kumwamba.+Tikanena za zinthu zazikulu zimene munachita,+Inu Mulungu, ndani angafanane ndi inu?+