Salimo 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kuli kumwamba.+Kukhulupirika kwanu kwafika m’mitambo.+ Salimo 89:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+ Salimo 103:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+
89 Ndidzaimba mpaka kalekale za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+Ndidzalengeza ndi pakamwa panga ku mibadwomibadwo za kukhulupirika kwanu.+
11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+