Salimo 89:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ndanena kuti: “Kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhazikika mpaka kalekale.+Ndipo mwakhazikitsa kukhulupirika kwanu kumwamba.”+ Salimo 108:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwakukulu ndipo kwafika kumwamba,+Choonadi chanu chafika kuthambo.+
2 Pakuti ndanena kuti: “Kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhazikika mpaka kalekale.+Ndipo mwakhazikitsa kukhulupirika kwanu kumwamba.”+
4 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwakukulu ndipo kwafika kumwamba,+Choonadi chanu chafika kuthambo.+