Salimo 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kuli kumwamba.+Kukhulupirika kwanu kwafika m’mitambo.+ Salimo 57:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwakukulu ndipo kwafika kumwamba,+Choonadi chanu chafika kuthambo.+ Salimo 103:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+
10 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwakukulu ndipo kwafika kumwamba,+Choonadi chanu chafika kuthambo.+
11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+