Salimo 71:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+
22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+