Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Mateyu 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo amene anali m’ngalawamo anam’gwadira ndi kunena kuti: “Ndinudi Mwana wa Mulungu.”+ Machitidwe 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yomweyo anayamba kulalikira za Yesu m’masunagoge,+ kuti Ameneyu ndiye Mwana wa Mulungu. Aheberi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana. 1 Yohane 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense amene amavomereza kuti Yesu Khristu ndi Mwana wa Mulungu,+ amakhala wogwirizana ndi Mulungu ndipo Mulungu amakhala wogwirizana naye.+
7 Ndinene za lamulo la Yehova.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.
15 Aliyense amene amavomereza kuti Yesu Khristu ndi Mwana wa Mulungu,+ amakhala wogwirizana ndi Mulungu ndipo Mulungu amakhala wogwirizana naye.+