1 Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+
24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+