1 Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma inu, zimene munamva pachiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamvazo zikakhalabe mumtima mwanu, mudzapitirizanso kukhala ogwirizana ndi Mwana komanso Atate. 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:24 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 30
24 Koma inu, zimene munamva pachiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamvazo zikakhalabe mumtima mwanu, mudzapitirizanso kukhala ogwirizana ndi Mwana komanso Atate.