1 Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:24 Nsanja ya Olonda,1/15/1987, tsa. 30
24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+