Salimo 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Pakuti Yehova wamugwira dzanja.+ Mika 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mdani wanga,+ usasangalale chifukwa cha zimene zandichitikira. Ngakhale kuti ndagwa, ndidzadzuka ndithu.+ Ngakhale kuti ndili mumdima,+ Yehova adzakhala kuwala kwanga.+ 2 Akorinto 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Timazunzidwa, koma osati mochita kusowa kolowera.+ Timagwetsedwa pansi,+ koma sitiwonongedwa.+
8 Iwe mdani wanga,+ usasangalale chifukwa cha zimene zandichitikira. Ngakhale kuti ndagwa, ndidzadzuka ndithu.+ Ngakhale kuti ndili mumdima,+ Yehova adzakhala kuwala kwanga.+