Salimo 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Pakuti Yehova wamugwira dzanja.+ Miyambo 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 pakuti wolungama akhoza kugwa ngakhale nthawi 7 ndipo ndithu adzadzukanso.+ Koma anthu oipa, tsoka lidzawapunthwitsa.+
16 pakuti wolungama akhoza kugwa ngakhale nthawi 7 ndipo ndithu adzadzukanso.+ Koma anthu oipa, tsoka lidzawapunthwitsa.+