Mlaliki 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi ndani akudziwa zinthu zabwino zimene munthu angachite pa masiku ochepa a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Chifukwa ndi ndani angauze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa? Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Nsanja ya Olonda,2/15/1997, tsa. 11
12 Ndi ndani akudziwa zinthu zabwino zimene munthu angachite pa masiku ochepa a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Chifukwa ndi ndani angauze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?