Mlaliki 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndani angadziwe zabwino zimene munthu angachite pa moyo wake,+ masiku onse a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Pakuti ndani angamuuze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:12 Nsanja ya Olonda,2/15/1997, tsa. 11
12 Ndani angadziwe zabwino zimene munthu angachite pa moyo wake,+ masiku onse a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Pakuti ndani angamuuze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?+