Miyambo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakachuluka mawu sipalephera kukhala zolakwa,+ koma wodziwa kulamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+ Miyambo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+ koma pakamwa pa zitsiru pamasefukira mawu opusa.+
19 Pakachuluka mawu sipalephera kukhala zolakwa,+ koma wodziwa kulamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+
2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+ koma pakamwa pa zitsiru pamasefukira mawu opusa.+