Genesis 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu Wamphamvuyonse adzakudalitsa. Adzakupatsa ana ndipo adzawachulukitsa moti adzakhala mitundu yambiri ya anthu.+ Genesis 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+ Machitidwe 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Nthawi itayandikira, yakuti lonjezo likwaniritsidwe limene Mulungu anapereka kwa Abulahamu, mtundu wa anthu unakula ndi kuwonjezeka mu Iguputo.+
3 Mulungu Wamphamvuyonse adzakudalitsa. Adzakupatsa ana ndipo adzawachulukitsa moti adzakhala mitundu yambiri ya anthu.+
11 Mulungu anamuuzanso kuti: “Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse.+ Ubereke ndipo ukhale ndi ana ambiri. Mitundu ndi mafuko ambiri adzatuluka mwa iwe, ndipo mafumu adzatuluka m’chiuno mwako.+
17 “Nthawi itayandikira, yakuti lonjezo likwaniritsidwe limene Mulungu anapereka kwa Abulahamu, mtundu wa anthu unakula ndi kuwonjezeka mu Iguputo.+