Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano dzina lako silikhalanso Abulamu, m’malo mwake likhala Abulahamu, chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri.

  • Genesis 48:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndipo anandiuza kuti, ‘Ndidzakupatsa ana,+ ndipo mwa iwe mudzatuluka mitundu yambiri ya anthu.+ Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako kuti lidzakhale dziko lawo mpaka kalekale.’+

  • Maliko 15:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo, kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Ngakhale amene anapachikidwa naye limodziwo analinso kumunyoza.+

  • Yohane 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 anatenga nthambi za kanjedza+ ndi kutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti:+ “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova,+ amenenso ndi mfumu+ ya Isiraeli!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena