Mateyu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+ Maliko 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno amene anali patsogolo ndi amene anali kubwera m’mbuyo anali kufuula kuti: “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!+
9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+
9 Ndiyeno amene anali patsogolo ndi amene anali kubwera m’mbuyo anali kufuula kuti: “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!+