Salimo 118:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wodala ndi Iye wobwera m’dzina la Yehova.+Takudalitsani anthu inu potuluka m’nyumba ya Yehova.+ Mateyu 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndithu ndikukuuzani, Kuyambira tsopano simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+ Luka 13:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano tamverani! Mulungu wachoka ndi kukusiyirani nyumba* yanuyi.+ Ndithu ndikukuuzani, simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+ Yohane 5:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndabwera m’dzina la Atate wanga,+ ndipo simunandilandire, koma wina akanabwera m’dzina lake, mukanamulandira ameneyo. Yohane 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 anatenga nthambi za kanjedza+ ndi kutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti:+ “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova,+ amenenso ndi mfumu+ ya Isiraeli!”
39 Ndithu ndikukuuzani, Kuyambira tsopano simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+
35 Tsopano tamverani! Mulungu wachoka ndi kukusiyirani nyumba* yanuyi.+ Ndithu ndikukuuzani, simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+
43 Ndabwera m’dzina la Atate wanga,+ ndipo simunandilandire, koma wina akanabwera m’dzina lake, mukanamulandira ameneyo.
13 anatenga nthambi za kanjedza+ ndi kutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti:+ “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova,+ amenenso ndi mfumu+ ya Isiraeli!”