Mateyu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+ Mateyu 23:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ndithu ndikukuuzani, Kuyambira tsopano simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+ Maliko 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno amene anali patsogolo ndi amene anali kubwera m’mbuyo anali kufuula kuti: “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!+ Luka 19:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+
9 Koma khamu la anthu, limene linali patsogolo pake ndi m’mbuyo mwake linali kufuula kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!*+ M’pulumutseni kumwambamwambako!”+
39 Ndithu ndikukuuzani, Kuyambira tsopano simudzandionanso kufikira pamene mudzanene kuti, ‘Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!’”+
9 Ndiyeno amene anali patsogolo ndi amene anali kubwera m’mbuyo anali kufuula kuti: “M’pulumutseni!+ Wodalitsidwa iye wobwera m’dzina la Yehova!+
38 Iwo anali kunena kuti: “Wodalitsidwa Iye wobwera monga Mfumu m’dzina la Yehova!+ Mtendere kumwamba, ndi ulemerero kumwambamwambako!”+