Salimo 118:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Haa! Inu Yehova, chonde tipulumutseni.+Haa! Inu Yehova, chonde tithandizeni kuti zinthu zitiyendere bwino.+ Mateyu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri
25 Haa! Inu Yehova, chonde tipulumutseni.+Haa! Inu Yehova, chonde tithandizeni kuti zinthu zitiyendere bwino.+
15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri