Maliko 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa anali kumuopa, pakuti khamu lonse la anthu nthawi zonse linali kudabwa ndi zimene anali kuphunzitsa.+
18 Ansembe aakulu ndi alembi anamva zimenezo, ndipo anayamba kufunafuna njira yomuphera,+ chifukwa anali kumuopa, pakuti khamu lonse la anthu nthawi zonse linali kudabwa ndi zimene anali kuphunzitsa.+