Mateyu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene Yesu anali kudutsa kuchokera kumeneko, anthu awiri akhungu+ anam’tsatira. Iwo anafuula ndi kunena kuti: “Mutichitire chifundo,+ Mwana wa Davide.” Mateyu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri
27 Pamene Yesu anali kudutsa kuchokera kumeneko, anthu awiri akhungu+ anam’tsatira. Iwo anafuula ndi kunena kuti: “Mutichitire chifundo,+ Mwana wa Davide.”
15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri