Mateyu 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+
30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+