Mateyu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene Yesu anali kudutsa kuchokera kumeneko, anthu awiri akhungu+ anam’tsatira. Iwo anafuula ndi kunena kuti: “Mutichitire chifundo,+ Mwana wa Davide.” Mateyu 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno kunabwera mayi wina wa ku Foinike+ kuchokera m’zigawo zimenezo ndi kufuula kuti: “Ndichitireni chifundo+ Ambuye, Mwana wa Davide. Mwana wanga wamkazi wagwidwa ndi chiwanda mochititsa mantha.” Maliko 10:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pamene anamva kuti ndi Yesu Mnazareti, Batimeyu anayamba kufuula kuti: “Mwana wa Davide,+ Yesu, ndichitireni chifundo!”+ Luka 18:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Atamva zimenezo anafuula kuti: “Yesu, Mwana wa Davide, ndichitireni chifundo!”+
27 Pamene Yesu anali kudutsa kuchokera kumeneko, anthu awiri akhungu+ anam’tsatira. Iwo anafuula ndi kunena kuti: “Mutichitire chifundo,+ Mwana wa Davide.”
22 Ndiyeno kunabwera mayi wina wa ku Foinike+ kuchokera m’zigawo zimenezo ndi kufuula kuti: “Ndichitireni chifundo+ Ambuye, Mwana wa Davide. Mwana wanga wamkazi wagwidwa ndi chiwanda mochititsa mantha.”
47 Pamene anamva kuti ndi Yesu Mnazareti, Batimeyu anayamba kufuula kuti: “Mwana wa Davide,+ Yesu, ndichitireni chifundo!”+