Mateyu 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+ Luka 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anafuula mokweza, kuti: “Yesu, Mlangizi,+ tichitireni chifundo!”
30 Ndiyeno amuna awiri akhungu anakhala pansi m’mphepete mwa msewu ndipo atamva kuti Yesu akudutsa, anafuula kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”+