Salimo 113:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akuchititsa mkazi wosabereka kukhala m’nyumba+Monga mayi wosangalala wa ana aamuna.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Salimo 116:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova ndi wachisomo ndi wolungama.+Mulungu wathu amasonyeza chifundo.+
9 Akuchititsa mkazi wosabereka kukhala m’nyumba+Monga mayi wosangalala wa ana aamuna.+Tamandani Ya, anthu inu!+