Salimo 112:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+ Salimo 117:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 117 Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu.+Mulemekezeni, inu mafuko onse.+
112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+