Yobu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Bwanji sindinafere m’chiberekero?+Bwanji sindinamwalire nditangotuluka m’mimba? Yeremiya 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 N’chifukwa chiyani ndinabadwa?+ Kodi ndinabadwa kuti ndidzagwire ntchito yakalavulagaga ndi kukhala wachisoni,+ ndi kuti moyo wanga ufike kumapeto kwake ndili wamanyazi?+
18 N’chifukwa chiyani ndinabadwa?+ Kodi ndinabadwa kuti ndidzagwire ntchito yakalavulagaga ndi kukhala wachisoni,+ ndi kuti moyo wanga ufike kumapeto kwake ndili wamanyazi?+