Yobu 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa munthu amene ali ndi mavuto,Ndiponso moyo kwa opwetekedwa mtima?+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+
20 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa munthu amene ali ndi mavuto,Ndiponso moyo kwa opwetekedwa mtima?+