Yeremiya 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+ Yeremiya 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 N’chifukwa chiyani sanandiphe ndili m’mimba kuti mayi anga akhale manda anga, ndiponso kuti akhale ndi pakati mpaka kalekale?+
10 Tsoka ine,+ chifukwa inu mayi anga munabereka ine munthu amene nthawi zonse ndimakangana ndipo ndimalimbana ndi dziko lonse.+ Sindinapereke ngongole komanso sanandikongoze kalikonse, koma anthu onse akunditemberera.+
17 N’chifukwa chiyani sanandiphe ndili m’mimba kuti mayi anga akhale manda anga, ndiponso kuti akhale ndi pakati mpaka kalekale?+