Yobu 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa silinatseke zitseko za mimba ya mayi anga,+Kuti ndisaone mavuto. Yobu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi munanditulutsiranji m’mimba?+Zikanakhala bwino ndikanafa kuti diso ndi limodzi lomwe lisandione.
18 Kodi munanditulutsiranji m’mimba?+Zikanakhala bwino ndikanafa kuti diso ndi limodzi lomwe lisandione.