Genesis 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehova ataona kuti Leya sanali kukondedwa kwenikweni, anam’patsa mphamvu zobereka,+ koma Rakele anali wosabereka.+ 1 Samueli 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma Hana anangom’patsa gawo limodzi. Komabe, iye anali kukonda kwambiri Hana+ ngakhale kuti Yehova anali atatseka mimba yake.+ Yobu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi munanditulutsiranji m’mimba?+Zikanakhala bwino ndikanafa kuti diso ndi limodzi lomwe lisandione.
31 Yehova ataona kuti Leya sanali kukondedwa kwenikweni, anam’patsa mphamvu zobereka,+ koma Rakele anali wosabereka.+
5 koma Hana anangom’patsa gawo limodzi. Komabe, iye anali kukonda kwambiri Hana+ ngakhale kuti Yehova anali atatseka mimba yake.+
18 Kodi munanditulutsiranji m’mimba?+Zikanakhala bwino ndikanafa kuti diso ndi limodzi lomwe lisandione.