Genesis 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zinatero pakuti Yehova anachititsa kuti akazi onse a m’nyumba ya Abimeleki asabereke, chifukwa cha Sara mkazi wa Abulahamu.+ Genesis 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yakobo anamupsera mtima kwambiri Rakele n’kumuyankha kuti:+ “Kodi ine ndine Mulungu amene akukulepheretsa kuberekayo?”+
18 Zinatero pakuti Yehova anachititsa kuti akazi onse a m’nyumba ya Abimeleki asabereke, chifukwa cha Sara mkazi wa Abulahamu.+
2 Pamenepo Yakobo anamupsera mtima kwambiri Rakele n’kumuyankha kuti:+ “Kodi ine ndine Mulungu amene akukulepheretsa kuberekayo?”+